Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Yakobo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.
28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+
13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.