Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ Yeremiya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?
9 “Mtima ndi wonyenga kwambiri kuposa china chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndani angaudziwe?