Yeremiya 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa inu.+ Iwo akungokupusitsani.* Iwo akulankhula masomphenya amumtima mwawo,+Osati ochokera mʼkamwa mwa Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:16 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 9
16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa inu.+ Iwo akungokupusitsani.* Iwo akulankhula masomphenya amumtima mwawo,+Osati ochokera mʼkamwa mwa Yehova.+