Yeremiya 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa makamu wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa anthu inu.+ Akukulimbikitsani kuchita zinthu zopanda pake.+ Iwo akulankhula masomphenya a mumtima mwawo+ osati ochokera m’kamwa mwa Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:16 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 9
16 Yehova wa makamu wanena kuti: “Musamvere mawu a aneneri amene akulosera kwa anthu inu.+ Akukulimbikitsani kuchita zinthu zopanda pake.+ Iwo akulankhula masomphenya a mumtima mwawo+ osati ochokera m’kamwa mwa Yehova.+