Salimo 115:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Mulungu wathu ali kumwamba.+Chilichonse chimene anafuna kuchita anachita.+ Yesaya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+ Ezekieli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako mzimu unanditenga+ ndipo kumbuyo kwanga ndinayamba kumva mawu amphamvu ngati chimkokomo chachikulu,+ akuti: “Utamandike ulemerero wa Yehova kumalo ake.”+
21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+
12 Kenako mzimu unanditenga+ ndipo kumbuyo kwanga ndinayamba kumva mawu amphamvu ngati chimkokomo chachikulu,+ akuti: “Utamandike ulemerero wa Yehova kumalo ake.”+