Yoswa 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova Mulungu wanu ndiye anali kuwathamangitsa pamaso panu,+ ndipo anawapitikitsa chifukwa cha inu. Pamenepo, inu munatenga malo awo monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulonjezerani.+ Nehemiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+
5 Yehova Mulungu wanu ndiye anali kuwathamangitsa pamaso panu,+ ndipo anawapitikitsa chifukwa cha inu. Pamenepo, inu munatenga malo awo monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulonjezerani.+
22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+