Ekisodo 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzawathamangitsa pamaso pako pang’onopang’ono kufikira mutaberekana ndi kulanda dzikolo.+ Ekisodo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Ekisodo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Koma inu sungani zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Deuteronomo 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova adzachotsa mitundu yonseyi chifukwa cha inu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+
2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
11 “Koma inu sungani zimene ndikukulamulani lero.+ Inetu ndikuthamangitsa pamaso panu Aamori, Akanani, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
23 Yehova adzachotsa mitundu yonseyi chifukwa cha inu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+