Deuteronomo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako,+ adzakuchotsera mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotsera Ahiti,+ Agirigasi,+ Aamori,+ Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi+ ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa iwe.+ Deuteronomo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova Mulungu wako adzakankhira mitundu imeneyi kutali ndi iwe, kuichotsa pamaso pako pang’onopang’ono.+ Sadzakulola kuifafaniza mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingakuchulukire ndi kukuwononga. Yoswa 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Kenako munawoloka Yorodano+ n’kufika ku Yeriko.+ Nzika za ku Yeriko, Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi, ndi Ayebusi anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka m’manja mwanu.+
7 “Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako,+ adzakuchotsera mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotsera Ahiti,+ Agirigasi,+ Aamori,+ Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi+ ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa iwe.+
22 “Yehova Mulungu wako adzakankhira mitundu imeneyi kutali ndi iwe, kuichotsa pamaso pako pang’onopang’ono.+ Sadzakulola kuifafaniza mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingakuchulukire ndi kukuwononga.
11 “‘Kenako munawoloka Yorodano+ n’kufika ku Yeriko.+ Nzika za ku Yeriko, Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi, ndi Ayebusi anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka m’manja mwanu.+