13 ‘Nyumba za mu Yerusalemu ndi nyumba za mafumu a Yuda zidzakhala zodetsedwa ngati malo ano a Tofeti.+ Zimenezi ndi nyumba zonse zimene pamadenga ake ankaperekapo nsembe kwa gulu lonse la zinthu zakuthambo+ ndi kuthirapo nsembe zachakumwa kwa milungu ina.’”+