Yeremiya 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo amangira Baala malo okwera kuti aziwotcha pamoto ana awo aamuna ngati nsembe zopsereza zathunthu zoperekedwa kwa Baala.+ Ine sindinawalamule zimenezi kapena kuzitchula ndipo sindinaziganizirepo mumtima mwanga.+
5 Iwo amangira Baala malo okwera kuti aziwotcha pamoto ana awo aamuna ngati nsembe zopsereza zathunthu zoperekedwa kwa Baala.+ Ine sindinawalamule zimenezi kapena kuzitchula ndipo sindinaziganizirepo mumtima mwanga.+