Yesaya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+ Yesaya 65:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa, Yeremiya 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Koma simunandimvere,’ watero Yehova, ‘ndipo munachita zimenezo n’cholinga chondikhumudwitsa ndi mafano anu. Zimenezi zakubweretserani tsoka.’+
8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+
3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa,
7 “‘Koma simunandimvere,’ watero Yehova, ‘ndipo munachita zimenezo n’cholinga chondikhumudwitsa ndi mafano anu. Zimenezi zakubweretserani tsoka.’+