2 Mbiri 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+ Yeremiya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Izi zachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene mwachita ndi kundikhumudwitsa nazo. Mwafukiza nsembe zautsi+ ndi kutumikira milungu ina imene inu kapena makolo anu simunaidziwe.+
25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+
3 Izi zachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene mwachita ndi kundikhumudwitsa nazo. Mwafukiza nsembe zautsi+ ndi kutumikira milungu ina imene inu kapena makolo anu simunaidziwe.+