Yeremiya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Izi zinachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene ankachita nʼkundikhumudwitsa nazo. Iwo ankapitiriza kupereka nsembe+ ndi kutumikira milungu ina imene inuyo, iwowo kapena makolo anu simunkaidziwa.+
3 Izi zinachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene ankachita nʼkundikhumudwitsa nazo. Iwo ankapitiriza kupereka nsembe+ ndi kutumikira milungu ina imene inuyo, iwowo kapena makolo anu simunkaidziwa.+