2 Mbiri 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 chifukwa chakuti andisiya+ nʼkumakapereka nsembe zautsi kwa milungu ina kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo, ndibweretsa mkwiyo wanga pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+
25 chifukwa chakuti andisiya+ nʼkumakapereka nsembe zautsi kwa milungu ina kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo, ndibweretsa mkwiyo wanga pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+