Yeremiya 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wa makamu, Wokubzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a m’nyumba ya Isiraeli+ ndi a m’nyumba ya Yuda achita ndi kundikhumudwitsa nazo pofukizira Baala nsembe zautsi.”+
17 “Yehova wa makamu, Wokubzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a m’nyumba ya Isiraeli+ ndi a m’nyumba ya Yuda achita ndi kundikhumudwitsa nazo pofukizira Baala nsembe zautsi.”+