Yeremiya 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi mizinda yake yonse yozungulira masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa khosi lawo kuti asamvere mawu anga.’”+
15 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi mizinda yake yonse yozungulira masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa khosi lawo kuti asamvere mawu anga.’”+