Salimo 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+ Yesaya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye analima mundawo n’kuchotsamo miyala, kenako anabzalamo mphesa zofiira zabwino kwambiri. Anamanga nsanja pakati pa mundawo.+ Anasemamonso choponderamo mphesa.+ Iye anali kuyembekezera kuti mundawo ubereka mphesa zabwino,+ koma unabereka mphesa zam’tchire.+ Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+
2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+
2 Iye analima mundawo n’kuchotsamo miyala, kenako anabzalamo mphesa zofiira zabwino kwambiri. Anamanga nsanja pakati pa mundawo.+ Anasemamonso choponderamo mphesa.+ Iye anali kuyembekezera kuti mundawo ubereka mphesa zabwino,+ koma unabereka mphesa zam’tchire.+
21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+