Mateyu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Mverani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ ndi kumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa ndi kumanga nsanja.+ Atatero anausiya m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina.+
33 “Mverani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ ndi kumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa ndi kumanga nsanja.+ Atatero anausiya m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina.+