Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 73:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iwo amanyodola ndi kulankhula zinthu zoipa.+

      Amalankhula za chinyengo chawo modzikweza.+

  • Ezekieli 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anandiyankha kuti: “Zolakwa za nyumba ya Isiraeli ndi Yuda+ n’zazikulu kwambiri.+ Dziko lawo ladzaza ndi magazi okhetsedwa,+ ndipo mumzindamo mwadzaza zaukathyali,+ pakuti iwo akunena kuti, ‘Yehova wachokamo m’dziko muno,+ ndipo Yehova sakuona.’+

  • Malaki 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Inu mwandinenera mawu achipongwe,”+ watero Yehova.

      Koma mukunena kuti: “Ife takunenerani zachipongwe zotani?”+

  • Mateyu 12:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu pa mawu alionse opanda pake amene iwo amalankhula.+

  • Yuda 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kudzapereka chiweruzo kwa onse,+ ndi kudzagamula kuti onse osaopa Mulungu apezeka ndi mlandu chifukwa cha ntchito zawo zonyoza Mulungu zimene anazichita mosaopa Mulungu, komanso chifukwa cha zinthu zonse zonyoza koopsa zimene ochimwa osaopa Mulungu anamunenera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena