Salimo 53:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa, ndipo amachita zinthu zonyansa zogwirizana ndi kupanda chilungamo kwawo.+Palibe amene akuchita zabwino.+ 2 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.
53 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa, ndipo amachita zinthu zonyansa zogwirizana ndi kupanda chilungamo kwawo.+Palibe amene akuchita zabwino.+
18 Pakuti amalankhula mawu odzitukumula opanda pake, ndipo pogwiritsa ntchito zilakolako za thupi+ komanso makhalidwe otayirira, amakopa+ amene akungopulumuka+ kumene kwa anthu ochita zolakwa.