Salimo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Onse apatuka,+ ndipo onsewo ndi achinyengo.+Palibe aliyense amene akuchita zabwino,+Palibiretu ndi mmodzi yemwe.+ Aroma 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Palibe munthu wolungama ndi mmodzi yemwe.+
3 Onse apatuka,+ ndipo onsewo ndi achinyengo.+Palibe aliyense amene akuchita zabwino,+Palibiretu ndi mmodzi yemwe.+