Mlaliki 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zimene ndapeza n’zakuti, Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha njira zina zambirimbiri.”+
29 Zimene ndapeza n’zakuti, Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha njira zina zambirimbiri.”+