Yesaya 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+
6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+