Genesis 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma dziko lapansi linali litaipa pamaso pa Mulungu woona,+ ndipo linadzaza ndi chiwawa.+ Levitiko 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero muzisunga malamulo anga kuti musamachite iliyonse mwa miyambo yonyansa imene anthu akhala akuchita inu musanafike.+ Pamenepo mudzapewa kudzidetsa ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’” Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+
30 Chotero muzisunga malamulo anga kuti musamachite iliyonse mwa miyambo yonyansa imene anthu akhala akuchita inu musanafike.+ Pamenepo mudzapewa kudzidetsa ndi miyamboyo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+