Machitidwe 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku m’badwo wopotoka maganizo uno.”+
40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku m’badwo wopotoka maganizo uno.”+