Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+

      Si ana ake, chilemacho n’chawo.+

      Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+

  • Salimo 78:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+

      M’badwo wosamva ndi wopanduka,+

      M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+

      Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+

  • Agalatiya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye anadzipereka chifukwa cha machimo athu,+ kuti atilanditse ku nthawi* yoipayi,+ mogwirizana ndi chifuniro+ cha Mulungu ndi Atate wathu.

  • Afilipi 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena