Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anayamba kuputa nsanje+ yake ndi milungu yachilendo.+

      Anapitiriza kumukhumudwitsa ndi zinthu zonyansa.+

  • 2 Mafumu 17:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo anapitiriza kuwotcha* pamoto+ ana awo aamuna ndi aakazi, kulosera+ ndi kuwombeza.*+ Anapitirizanso+ kuchita zoipa* pamaso pa Yehova ndi cholinga chomukwiyitsa.+

  • 2 Mafumu 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa chakuti andisiya n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho mkwiyo wanga wayakira malo ano ndipo suzimitsidwa.’”’+

  • Yeremiya 32:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu a mumzindawu abwera kudzayatsa moto mzindawu kuti upseretu.+ Ayatsanso nyumba zawo chifukwa pamadenga ake amafukizirapo nsembe zautsi kwa Baala ndipo amathira nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+

  • Yeremiya 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘Ana a Isiraeli ndi ana a Yuda akhala akuchita zoipa pamaso panga kuyambira pa ubwana wawo.+ Ana a Isiraeli akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena