Ekisodo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+ 1 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+
14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+
30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+