2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ 2 Mbiri 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+ Yeremiya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Akasidi adzabweranso ndithu kudzamenyana ndi mzinda uno, kuulanda ndi kuutentha ndi moto.”+ Yeremiya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+ Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+
13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+
11 Yehova wasonyeza ukali wake wonse.+ Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+Iye wayatsa moto m’Ziyoni, umene wanyeketsa maziko ake.+