2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Salimo 74:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo atentha malo anu opatulika.+Aipitsa ndi kugwetsera pansi chihema chokhala ndi dzina lanu.+ Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+