Yeremiya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinalankhula nawe pamene unali pa ufulu,+ koma iwe unandiyankha kuti, ‘Sindidzamvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata, moti sunamvere mawu anga.+ Ezekieli 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akazi amenewa anayamba kuchita uhule m’dziko la Iguputo.+ Anayamba uhule umenewu ali atsikana ang’onoang’ono.+ Kumeneko amuna anafinya mabere awo+ ndi kutsamira chifuwa chawo ali anamwali.
21 Ndinalankhula nawe pamene unali pa ufulu,+ koma iwe unandiyankha kuti, ‘Sindidzamvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata, moti sunamvere mawu anga.+
3 Akazi amenewa anayamba kuchita uhule m’dziko la Iguputo.+ Anayamba uhule umenewu ali atsikana ang’onoang’ono.+ Kumeneko amuna anafinya mabere awo+ ndi kutsamira chifuwa chawo ali anamwali.