31 Inu anthu a m’badwo uwu, ganizirani mawu a Yehova.+
“Kodi ndangokhala ngati chipululu kwa Isiraeli+ kapena ngati dziko la mdima wandiweyani? N’chifukwa chiyani anthu angawa anena kuti, ‘Takhala tikuyendayenda mmene tikufunira. Sitibwereranso kwa inu’?+