Salimo 78:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sanasunge pangano la Mulungu,+Ndipo anakana kutsatira chilamulo chake.+ Yesaya 42:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndani wachititsa kuti Yakobo angokhala zofunkha ndiponso kupereka Isiraeli kwa anthu olanda? Kodi si Yehova amene iwo am’chimwira, amene sanafune kuyenda m’njira zake ndipo sanasunge malamulo ake?+ Yeremiya 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ife sitimvera mawu amene watiuza m’dzina la Yehova.+
24 Ndani wachititsa kuti Yakobo angokhala zofunkha ndiponso kupereka Isiraeli kwa anthu olanda? Kodi si Yehova amene iwo am’chimwira, amene sanafune kuyenda m’njira zake ndipo sanasunge malamulo ake?+