Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ 2 Mbiri 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthuwo anagonjetsana chifukwa anaukirana okhaokha. Fuko limodzi linkamenyana ndi fuko lina+ ndiponso mzinda ndi mzinda wina, popeza Mulungu anawasiya pa chisokonezo ndi zowawa zosiyanasiyana.+ Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
6 Anthuwo anagonjetsana chifukwa anaukirana okhaokha. Fuko limodzi linkamenyana ndi fuko lina+ ndiponso mzinda ndi mzinda wina, popeza Mulungu anawasiya pa chisokonezo ndi zowawa zosiyanasiyana.+
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+