15 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu, zoyambirira ndi zomalizira,+ zinalembedwa m’mawu a mneneri Semaya+ ndiponso m’mawu a Ido+ wamasomphenya, motsatira mndandanda wa mayina a makolo. Nthawi zonse panali kuchitika nkhondo pakati pa Rehobowamu+ ndi Yerobowamu.+