2 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’mawu a mneneri Natani.+ Zalembedwanso mu ulosi wa Ahiya+ Msilo,+ ndiponso m’buku la masomphenya a Ido+ wamasomphenya, lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati.+ 2 Mbiri 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nkhani zina zokhudza Abiya, njira zake ndi mawu ake, zinalembedwa m’buku la ndemanga la mneneri Ido.+
29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’mawu a mneneri Natani.+ Zalembedwanso mu ulosi wa Ahiya+ Msilo,+ ndiponso m’buku la masomphenya a Ido+ wamasomphenya, lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati.+
22 Nkhani zina zokhudza Abiya, njira zake ndi mawu ake, zinalembedwa m’buku la ndemanga la mneneri Ido.+