Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+

  • 2 Samueli 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Natani atafika kwa Davide+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene anali kukhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.

  • 1 Mafumu 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.

  • 1 Mafumu 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?

  • 1 Mafumu 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Nthawi yomweyo Mfumu Davide inati: “Amuna inu, ndiitanireni wansembe Zadoki,+ mneneri Natani ndi Benaya+ mwana wa Yehoyada.” Anthuwo anabweradi.

  • 1 Mbiri 29:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena