2 Mbiri 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yerobowamu sanakhalenso ndi mphamvu+ m’masiku a Abiya, ndipo Yehova anamukantha+ moti anafa.