1 Samueli 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Patapita masiku 10, Yehova anakantha+ Nabala ndipo anafa. 2 Samueli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Natani anapita kunyumba kwake. Ndiyeno Yehova anakantha+ mwana amene mkazi wa Uriya anaberekera Davide, moti mwanayo anayamba kudwala. 1 Mafumu 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Nadabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. Machitidwe 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.
15 Kenako Natani anapita kunyumba kwake. Ndiyeno Yehova anakantha+ mwana amene mkazi wa Uriya anaberekera Davide, moti mwanayo anayamba kudwala.
20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Nadabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.