2 Mbiri 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yerobowamu sanakhalenso ndi mphamvu+ m’masiku a Abiya, ndipo Yehova anamukantha+ moti anafa. Yobu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu nawonso amagona pansi osadzuka.+Sadzadzuka mpaka kumwamba kutachoka,+Sadzadzutsidwa ku tulo tawo.+
12 Anthu nawonso amagona pansi osadzuka.+Sadzadzuka mpaka kumwamba kutachoka,+Sadzadzutsidwa ku tulo tawo.+