1 Mafumu 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nadabu+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka chachiwiri cha Asa mfumu ya Yuda, ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli kwa zaka ziwiri.
25 Nadabu+ mwana wa Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka chachiwiri cha Asa mfumu ya Yuda, ndipo anapitiriza kulamulira Isiraeli kwa zaka ziwiri.