1 Mafumu 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Nadabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Nadabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.