Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+

  • 1 Mafumu 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka, udzisinthe+ kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu ndipo upite ku Silo. Kumeneko n’kumene kuli mneneri Ahiya.+ Ameneyo ndiye anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+

  • 1 Mafumu 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa chifukwa chimenechi, ndibweretsa tsoka panyumba ya Yerobowamu. Ndithu ndidzapha munthu aliyense wokodzera khoma*+ wa m’nyumba ya Yerobowamu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.+ Komanso ndidzaseseratu nyumba ya Yerobowamu,+ monga momwe munthu amasesera ndowe mpaka atakazitaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena