11 Iye atangokhala pampando wachifumu n’kuyamba kulamulira, anapha anthu onse a m’nyumba ya Basa. Sanasiye ndi moyo munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Basa kapena abale ake amene akanatha kubwezera magazi ake,+ kapenanso anzake.
8 Nyumba yonse ya Ahabu+ ifafanizidwe. Ine ndidzapha munthu aliyense wokodzera khoma*+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale aliyense wonyozeka ndi wopanda pake+ mu Isiraeli.