1 Samueli 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Mulungu alange mowirikiza+ adani a Davide, ngati ine ndidzasiya munthu aliyense wa m’nyumba ya Nabala wokodzera khoma*+ ali wamoyo kufikira m’mawa.”+
22 Choncho Mulungu alange mowirikiza+ adani a Davide, ngati ine ndidzasiya munthu aliyense wa m’nyumba ya Nabala wokodzera khoma*+ ali wamoyo kufikira m’mawa.”+