13 Yehova andilange ine Yonatani mowirikiza,+ ndikadziwa kuti bambo anga akufuna kukuchitira choipa koma osakudziwitsa ndi kukulola kuti uchoke, moti iweyo n’kulepheradi kuchoka mwamtendere. Yehova akhale nawe+ monga mmene anakhalira ndi bambo anga.+