Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 38:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+

  • 1 Samueli 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Motero amuna a Isiraeli anatopa kwambiri pa tsiku limenelo, komabe Sauli analumbirira+ anthuwo kuti: “Munthu aliyense wodya mkate dzuwa lisanalowe, komanso ndisanabwezere+ adani anga, ndi wotembereredwa!” Choncho panalibe aliyense mwa anthuwo amene anadya mkate.+

  • 2 Samueli 12:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Davide atamva zimenezi anamukwiyira kwambiri munthuyo,+ moti anauza Natani kuti: “Ndithu, pali Yehova Mulungu wamoyo,+ munthu wochita zimenezi ayenera kufa!+

  • Yakobo 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena