Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Ukapereka lonjezo kwa Yehova+ Mulungu wako usachedwe kulikwaniritsa kuopera kuti ungachimwe,+ chifukwa Yehova Mulungu wako adzafuna ndithu kuti ukwaniritse chimene walonjezacho.+

  • Oweruza 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno iye anapempha amuna a ku Sukoti+ kuti: “Chonde, patsaniko anthu amene akunditsatirawa+ mitanda yobulungira ya mkate chifukwa ndi otopa, pakuti ndikuthamangitsa Zeba+ ndi Zalimuna,+ mafumu a Midiyani.”

  • 2 Samueli 17:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iwo anabweretsanso uchi,+ mafuta a mkaka,+ wa ng’ombe ndiponso nkhosa. Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo anali kunena kuti: “Anthu amenewa ali ndi njala, atopa ndipo ali ndi ludzu m’chipululu.”+

  • Salimo 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+

      Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+

      Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena