Miyambo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+ Machitidwe 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anthu olankhula chinenero chachilendo kumeneko anatisonyeza kukoma mtima kwapadera.+ Iwo anasonkha moto ndi kutilandira bwino tonse chifukwa kunali kugwa mvula ndiponso kuzizira.+
25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+
2 Ndipo anthu olankhula chinenero chachilendo kumeneko anatisonyeza kukoma mtima kwapadera.+ Iwo anasonkha moto ndi kutilandira bwino tonse chifukwa kunali kugwa mvula ndiponso kuzizira.+