Miyambo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wopereka mowolowa manja zinthu zidzamuyendera bwino,*+Ndipo amene amatsitsimula ena* nayenso adzatsitsimulidwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:25 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 30
25 Munthu wopereka mowolowa manja zinthu zidzamuyendera bwino,*+Ndipo amene amatsitsimula ena* nayenso adzatsitsimulidwa.+